2 Mbiri 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo ndidzakhazikitsa mpando wacifumu wa ufumu wako, monga ndinapangana ndi Davide atate wako, ndi kuti, Sadzakusowa munthu wokhala mfumu m'Israyeli.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:11-22