2 Mbiri 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anthu anga ochedwa dzina langa akadzicepetsa, nakapemphera, nakafuna nkhope yanga, nakatembenuka kuleka njira zao zoipa; pamenepo ndidzamvera m'Mwamba, ndi kukhululukira coipa cao, ndi kuciritsa dziko lao.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:4-15