2 Mbiri 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anaonekera kwa Solomo usiku, nanena naye, Ndamva pemphero lako, ndadzisankhira malo ano akhale nyumba ya nsembe.

2 Mbiri 7

2 Mbiri 7:11-16