2 Mbiri 6:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano nyamukani, Yehova Mulungu, kudza kopumulira kwanu, Inu ndi likasa la mphamvu yanu; ansembe anu, Yehova Mulungu, abvale cipulumutso; ndi okondedwa anu akondwere nazo zabwino.

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:32-42