2 Mbiri 6:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akabwerera kwa Inu ndi mtima wao wonse, ndi moyo wao wonse, m'dziko la undende wao, kumene adawatengera andende; nakapemphera kuloza ku dziko lao limene munapatsa makolo ao, ndi mudzi mudausankha, ndi kunyumba ndamangira dzina lanuyi;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:29-42