2 Mbiri 6:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akacimwira Inu (pakuti palibe munthu wosacimwa), nimukakwiya nao, ndi kuwapereka kwa adani, kuti awatenge andende kumka nao ku dziko lakutali, kapena lapafupi;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:34-38