2 Mbiri 6:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso kunena za mlendo wosakhala wa anthu anu Israyeli, akafumira ku dziko lakutari cifukwa ca dzina lanu lalikuru, ndi dzanja lanu lamphamvu, ndi mkono wanu wotambasuka; akadza iwowa ndi kupemphera kuloza ku nyumba iyi;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:29-37