2 Mbiri 6:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukakhala njala m'dzikomo, mukakhala mliri, mukakhala cinsikwi, kapena cinoni, dzombe, kapena kapuce; akawamangira misasa adani ao, m'dziko la midzi yao; mukakhala mliri uli wonse, kapena nthenda iri yonse;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:20-31