2 Mbiri 6:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukatsekeka m'mwamba, mopanda mvula, cifukwa ca kukucimwirani; akapemphera iwo kuloza kumalo kuno, ndi kubvomereza dzina lanu, ndi kutembenuka kwa zoipa zao, pamene muwasautsa;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:19-27