2 Mbiri 6:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anu Israyeli akawakantha mdani cifukwa ca kukucimwirani, nakabwerera iwowa ndi kubvomereza dzina lanu, ndi kupemphera, ndi kupembedzera pamaso panu m'nyumba yino;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:23-33