2 Mbiri 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akacimwira mnansi wace, ndipo akamuikira lumbiro lakumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira ku guwa lanu la nsembe, m'nyumba yino;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:21-27