2 Mbiri 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kodi nzoona kuti Mulungu akhala ndi anthu pa dziko lapansi? taonani, thambo, inde m'mwambamwamba, sizifikira inu, koposa kotani nanga nyumba iyi ndaimanga?

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:10-20