2 Mbiri 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

inu amene mwasungira mtumiki wanu Davide atate wanga cija mudamlonjezaci: inde munanena ndi pakamwa panu, ndipo mwacita ndi dzanja lanu, monga momwe muli lero lino.

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:12-23