2 Mbiri 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe analowa nalo likasa la cipangano la Yehova kumalo kwace m'moneneramo mwa kacisi, m'malo opatulikitsa, pansi pa mapiko a akerubi.

2 Mbiri 5

2 Mbiri 5:6-9