2 Mbiri 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munalibe kanthu kena m'likasa, koma magome awiri Mose anawaika m'mwemo ku Horebu, muja Yehova anacita cipangano ndi ana a Israyeli poturuka iwo m'Aigupto.

2 Mbiri 5

2 Mbiri 5:8-14