2 Mbiri 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pansi pace panali mafanziro a ng'ombe zakulizinga khumi ku mkono umodzi, zakuzinga thawalelo pozungulira pace. Ng'ombezo zinali m'mizere iwiri, zinayengeka poyengedwa thawalelo.

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:1-6