2 Mbiri 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Miphika yomwe, ndi zoolera, ndi mitungo, ndi zipangizo zace zonse, Huramu Abi anazipangira mfumu Solomo, kuzipangira nyumba ya Yehova, za mkuwa wonyezimira.

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:9-22