2 Mbiri 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nsanamira ziwiri, ndi zikhozo, ndi mitu iwiri inali pamwamba pa nsanamirazo, ndi maukonde awiri akukuta zikho ziwiri za mitu iri pamwamba pa nsanamirazo,

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:9-13