2 Mbiri 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m'litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mikono khumi.

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:1-3