2 Mbiri 36:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti akwaniridwe mau a Yehova pakamwa pa Yeremiya, mpaka dziko linakondwera nao masabata ace; masiku onse a kupasuka kwace linasunga sabata, kukwaniritsa zaka makumi asanu ndi awiri.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:11-23