2 Mbiri 36:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zipangizo zonse za nyumba ya Mulungu, zazikuru ndi zazing'ono, ndi cuma ca nyumba ya Yehova, ndi cuma ca mfumu, ndi ca akalonga ace, anabwera nazo zonsezi ku Babulo.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:13-22