2 Mbiri 35:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo kutumikira konse kwa Yehova kunakonzeka tsiku lomwelo, kucita Paskha, ndi kupereka nsembe zopsereza pa guwa la nsembe la Yehova, monga analamulira mfumu Yosiya.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:8-19