2 Mbiri 35:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacotsapo nsembe zopsereza, kuti azipereke kwa ana a anthu monga mwa magawidwe a nyumba za makolo; azipereke kwa Yehova monga mulembedwa m'buku la Mose. Natero momwemo ndi ng'ombezo.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:6-18