2 Mbiri 34:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nikwera mfumu ku nyumba ya Yehova ndi amuna onse a m'Yuda, ndi okhala m'Yerusalemu, ndi ansembe ndi Alevi, ndi anthu onse akuru ndi ang'ono; nawerenga iye m'makutu mwao mau onse a buku la cipangano adalipeza m'nyumba ya Yehova.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:23-33