2 Mbiri 34:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ndidzakusonkhanitsa ku makolo ako, nudzaikidwa kumanda kwako mumtendere, ndi maso ako sadzapenya zoipa zonse ndidzafikitsira malo ano ndi okhala m'mwemo. Ndipo anambwezera mfumu mau.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:21-31