2 Mbiri 34:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Safani mlembi anauza mfumu, ndi kuti, Hilikiya wansembe anandipatsa buku. Nawerengamo Safani pamaso pa mfumu.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:8-25