2 Mbiri 34:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hilikiya anayankha nati kwa Safani mlembi, Ndapeza buku la cilamulo m'nyumba ya Yehova. Hilikiya napereka buku kwa Safani.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:13-23