2 Mbiri 34:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anayang'aniranso osenza akatundu, nafulumiza onse akugwira nchito ya utumiki uli wonse; ndi mwa Alevi munali alembi, ndi akapitao, ndi odikira.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:7-20