2 Mbiri 33:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapititsanso ana ace pamoto m'cigwa ca ana a Hinomu, naombeza maula, nasamalira malodza, nacita zanyanga, naika obwebweta ndi openduza; anacita zoipa zambiri pamaso pa Yehova kuutsa mkwiyo wace.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:1-16