2 Mbiri 33:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita coipa pamaso pa Yehova, monga umo anacitira Manase atate wace; pakuti Amoni anaphera nsembe mafano osema onse amene adawapanga Manase atate wace, nawatumikira.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:18-25