2 Mbiri 33:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacotsa milungu yacilendo, ndi fanoli m'nyumba ya Yehova, ndi maguwa onse a nsembe anawamanga m'phiri la nyumba ya Yehova ndi m'Yerusalemu, nawataya kunja kwa mudzi.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:9-19