2 Mbiri 33:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anampempha, ndipo anapembedzeka, namvera kupembedza kwace, nambwezera ku Yerusalemu m'ufumu wace. Pamenepo anadziwa Manase kuti Yehova ndiye Mulungu.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:11-19