2 Mbiri 33:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Yehova anawafikitsira akazembe a khamu la nkhondo la mfumu ya Asuri, namgwira Manase ndi zokowera, nammanga matangadza, namuka naye ku Babulo.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:7-13