2 Mbiri 32:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analimbika mtima, namangitsa linga lonse mopasuka, nalikweza mpaka pansanja, ndi linga lina kunja kwace, nalimbitsa Milo m'mudzi wa Davide, napanga zida ndi zikopa zocuruka.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:3-11