2 Mbiri 31:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi iwo oyesedwa mwa cibadwidwe ca ansembe mwa nyumba za makolo ao, ndi Alevi, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu m'udikiro mwao, monga mwa zigawo zao;

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:9-19