2 Mbiri 31:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Kore mwana wa Imna Mlevi, wa ku cipata ca kum'mawa, anayang'anira zopereka zaufulu za Mulungu, kugawira nsembe zokweza za Yehova, ndi zopatulikitsa.

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:8-20