2 Mbiri 30:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero anakhazikitsa mau kulalikira mwa Israyeli lonse, kuyambira Beereseba kufikira ku Dani, kuti abwere kucitira Yehova Mulungu wa Israyeli Paskha ku Yerusalemu; pakuti nthawi yaikuru sanacita monga mudalembedwa.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:4-8