2 Mbiri 30:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo munali cimwemwe cacikuru m'Yerusalemu; pakuti kuyambira masiku a Solomo mwana wa Davide mfumu ya Israyeli simunacitika cotero m'Yerusalemu.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:23-27