2 Mbiri 30:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo msonkhano wonse unapangana kucita masiku asanu ndi awiri ena, nacita masiku asanu ndi awiri ena ndi cimwemwe.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:18-25