2 Mbiri 30:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti munali ambiri mumsonkhano sanadzipatula; potero Alevi anayang'anira kupha za Paskha kwa ali yense wosakhala woyera, kuwapatulira Yehova.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:10-22