2 Mbiri 30:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi waciwiri, ndipo ansembe ndi Alevi anacita manyazi, nadzipatula, nabwera nazo nsembe zopsereza ku nyumba ya Yehova.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:9-19