2 Mbiri 30:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya anatumiza kwa Israyeli ndi Yuda onse, nalembanso akalata kwa Efraimu ndi Manase, kuti abwere ku nyumba ya Yehova ku Yerusalemu, kucitira Yehova Mulungu wa Israyeli Paskha.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:1-7