2 Mbiri 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Napanga maunyolo onga a m'moneneramo, nawamanga pa mitu ya nsanamirazi, napanga makangaza zana limodzi, nawamanga pamaunyolo.

2 Mbiri 3

2 Mbiri 3:11-17