2 Mbiri 29:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika Alevi m'nyumba ya Yehova ndi nsanje, ndi zisakasa, ndi azeze, monga umo adauzira Davide, ndi Gadi mlauli wa mfumu, ndi Natani mneneriyo; pakuti lamulo ili lidafuma kwa Yehova mwa aneneri ace.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:16-27