2 Mbiri 29:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anapha ng'ombezo, ndi ansembe analandira mwazi, nauwaza pa guwa la nsembe, napha nkhosa zamphongozo, nawaza mwazi pa guwa la nsembe; anaphanso ana a nkhosawo, nawaza mwazi pa guwa la nsembe.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:18-28