2 Mbiri 29:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana anga, musazengereza tsopano; popeza Yehova anakusankhani inu muime pamaso pace, kumtumikira Iye, ndi kuti mukhale atumiki ace ndi kufukiza zonunkhira.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:10-13