2 Mbiri 28:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Peka mwana wa Remaliya anapha ku Yuda tsiku limodzi zikwi zana limodzi ndi makumi awiri, ngwazi zonsezo; popeza adasiya Yehova Mulungu wa makolo ao.

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:5-13