2 Mbiri 28:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza anaphera nsembe milungu ya Damasiko yomkantha, nati, Popeza milungu ya mafumu a Aramu iwathandiza, ndiiphere nsembe, indithandize inenso. Koma inamkhumudwitsa iye, ndi Aisrayeli onse.

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:14-27