2 Mbiri 28:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akuru ena a ana a Efraimu, Azariya mwana wa Yohanana, Berekiya mwana wa Mesilemoti, ndi Yehizikiya mwana wa Salumu, ndi Amasa mwana wa Hadilai, anaukira aja ofuma kunkhondo,

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:9-20