2 Mbiri 28:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi; koma sanacita zoongoka pamaso pa Yehova ngati Davide kholo lace,

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:1-9